Samandisiya ndekha
Amandigwila nkono
Samandisiya ndekha
Amandigwila nkono
Nangula
Pakati panamondwe
Pakati pazovuta zamoyo
Nangula wanga ndinu Yehova
Nangula wanga ndinu Yehova
Chorus
Chigwa cham'dimamo muli nane
Namondwe adze mumayenda nane
Chigwa cham'dimamo muli nane
Nangula
Yesu nangula wanga
Chigwa cham'dimamo muli nane
Namondwe adze mumayenda nane
Chigwa cham'dimamo muli nane
Nangula (Yeaha)
Yesu nangula wamoyo
Samandisiya ndekha
Amandigwila nkono
Samandisiya ndekha
Amandigwila nkono
Chifukwa malonjezo anu ali inde ndi amen (ndi amen)
Jehova Jireh moyo wanga usamaleni (usamaleni)
Please be my anchor and hold me down (every time)
While enemies around me are ganging up
Poti pothawila panga ndinu (ndinu)
Tanthwe lolimba ndinu
Nangula wangaso ndinu Yahweh (ndinu)
Nyimboyi ndaimbila inu
Ndipo kuchoka kumwamba
Kufika pansi pantambo
Kulibe wina wayenela matamando
Landilani Ulemu wanu Yahweh
Simchita mantha poti m'nandiuza nokha kuti
Chigwa cham'dimamo muli nane (nane ine)
Namondwe adze mumayenda nane (namondwe adze muli nane)
Chigwa cham'dimamo muli nane
Nangula (munati muli nane eeh)
Yesu nangula wanga
Chigwa cham'dimamo muli nane (muli nane ine)
Namondwe adze mumayenda nane (namondwe adze muli nane)
Chigwa cham'dimamo muli nane
Nangula (nane nane nane)
Yesu nangula wamoyo
Samandisiya ndekha
Amandigwila nkono
Samandisiya ndekha
Amandigwila nkono
Nangula
Nangula
Yesu nangula wamoyo